16/11/2024
Ma guyz awawa ndye asowa hvy kom tyesesa kuwapeza tiwafuse chomwe asakuyimbla limodzi komaso chomwe asatulutsa nyimbo za nyuwani kuti tziwe Zfukwa zawo.๐ต๐ต
Ndye guys tyambe ndan kufutsa pamenepa tuzen๐๐๐๐๐พ๐
1.Real Jay
2.Puxy
3.Gibo okay
4.Wes Kay