Boyd Lucky Mogha

Boyd Lucky Mogha Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Boyd Lucky Mogha, Flea Market, Lilongwe.

29/01/2024

ULADI M***A ANATHERA KU NDENDE CHIFUKWA CHA UMBAVA WA MA PASSPORT. LERO WAJOINA MBAVA ZA CONGRESS. RUBBISH BELONGS TO THE DUSTBINS.

04/12/2023
04/12/2023
You can order quality tomatoes  at K45,000 per dish in Chitedze Lilongwe. Call 0999178809
04/04/2023

You can order quality tomatoes at K45,000 per dish in Chitedze Lilongwe. Call 0999178809

Mbava zobera kuzera pa kapinga wa ku Statehouse, zoona mpaka 1billion for kapinga maintenance?
03/04/2023

Mbava zobera kuzera pa kapinga wa ku Statehouse, zoona mpaka 1billion for kapinga maintenance?

31/03/2023

Mkulu wina dzina lake Dandaula Mwalimbwe wa mmudzi wa Mwalimbwe, mfumu yaikulu Malili ku Lilongwe, ku dera la Chitedze, wazipha pozimangirira ndi linya ku denga la chipinda cha nyumba yogona alendo pa zifukwa za nkhawa ndi ngongole zimene anali nazo ndipo amakanika kuti abweze ndaramazo.
Zikumveka kuti asanadziphe mkuluyi anali atatenga ndarama zokwana K150,000 kuchokera kwa mkazi wake watsopano kuti akagule katundu wina woti adzigulitsa pa khomo koma bambowa anaononga ndarama yonseyi mu njira yosangalatsa azimayi enanso.

Anthu oti ali serious sakhala chonchi ngati akugawana uchitsiru pamene winayo diso lili tong'ooooo ngati wavala nyau.
29/03/2023

Anthu oti ali serious sakhala chonchi ngati akugawana uchitsiru pamene winayo diso lili tong'ooooo ngati wavala nyau.

Cyclone Gwengwe will never heal our malawi economy. Zonse zathera pa rent kuseriku.
26/03/2023

Cyclone Gwengwe will never heal our malawi economy. Zonse zathera pa rent kuseriku.

20/03/2023

The legend of love, passion and humanity is gone. DD Sunshine founder and coach, David Dube has just been buried but his exceptional legacy still lives. DD Sunshine players paying their final respect to the champion of women football.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Boyd Lucky Mogha posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Boyd Lucky Mogha:

Share

Category