Ansate Communication

Ansate Communication Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ansate Communication, Shopping & retail, @ communication, Lilongwe.

We are the best and no one can argue, try us today to comfirm our claim.Ndife akadawulo ndipo palibe angatsutse za zimen...
16/02/2026

We are the best and no one can argue, try us today to comfirm our claim.

Ndife akadawulo ndipo palibe angatsutse za zimenezi, Tiyeseni Lero kuti mudzionere nokha pakudzitamandira kwathu.

Ansante investment and general delear
Ndi ife simudzakhumudwa

call /wap

0739256773
0995334650

mwai ulipo sopano oti m***a kutumidza ndalama around south Africa kapena kunja kwa ziko lino ngati Ethiopia,, Nigeria,, ...
02/02/2026

mwai ulipo sopano oti m***a kutumidza ndalama around south Africa kapena kunja kwa ziko lino ngati Ethiopia,, Nigeria,, Zimbabwe,,, GANA,,,,kungodzi ziko lonse tikufika

tilankhuleni kuti tikuthandizeni

ndi Ansante investment njila yokhayo yodalilika

0995334650

0739256773

Ansante investment and general delear only way to success

Mwedzi omwe anthu ambiri amaulila ndiumeneu wa February koma ndi ife a Ansate investment mwedzi umeneu utha kukhala mwed...
02/02/2026

Mwedzi omwe anthu ambiri amaulila ndiumeneu wa February

koma ndi ife a Ansate investment mwedzi umeneu utha kukhala mwedzi wanu wamayankho ndi mdalitso

simudachedwe tilankhuleni pa

00265995334650

0027739256773

February wafika ndi mdalitso ndi chipambano painu

maservises athu amatheka muphindi zochepa ndipo timalemekedza kalikonse komwe mwatipasa

Ambuye akudaliseni khalani mgulu LA anthu osogola pangani like and share kuti nao ena apindule

anyamata ozisata mwazuka bwanji bwelani timvane kuno moyo mkamodziteam Ansate
25/01/2026

anyamata ozisata mwazuka bwanji bwelani timvane kuno moyo mkamodzi

team Ansate

mwaswera bwanji kumeneko agulu
24/01/2026

mwaswera bwanji kumeneko agulu

Goshen City Dedza Dynamos yafika mundime yamasemifainolo a Castel Challenge Cup itagonjetsa Ekhaya FC 2-0 pabwalo la Mpi...
24/01/2026

Goshen City Dedza Dynamos yafika mundime yamasemifainolo a Castel Challenge Cup itagonjetsa Ekhaya FC 2-0 pabwalo la Mpira ku Chiwembe mu nzinda wa Blantyre.

Luke Chima komanso Gift Magola anagolesera Dedza zomwe zachititsa kuti afike mundimeyi.

Anyamata a Alex Ngwira azakumana ndi opambana pakati pa Chitipa United komanso Blue Eagles FC mundime yotsatira.

Ndipo pamasewero ena, Mzuzu City Hammers yatulutsa Silver Strikers mumpikitsanowu itapambana 2-1 pabwalo la Rumphi chigawo chakumpoto.

Isaiah Nyirenda komanso Aubry Simbi anagolesera Hammers pomwe Innocent Shema anamwetsa chigoli cha ma Central Bankers.

Izi zikutanthauza kuti Hammers izakumana ndi Mighty Wanderers mundime ya makotafainolo kuchigawochi.


zathapo

Komatu mukanasankha chimodzi, zikachuluka sizidyeka.china chikutaikani apa ohhhhowAnsante anyamata arsenal mwazuka bwa
21/01/2026

Komatu mukanasankha chimodzi, zikachuluka sizidyeka.

china chikutaikani apa ohhhhow

Ansante
anyamata arsenal mwazuka bwa

Tikhale limodzi nthawi ikamati 22:00 ma gunners vs Liverpool Amaona ngati sikuda Ansante kufika posafukilika Tigona koma...
08/01/2026

Tikhale limodzi nthawi ikamati 22:00 ma gunners vs Liverpool

Amaona ngati sikuda

Ansante kufika posafukilika

Tigona koma mochedwerapo

Just follow Ansante for more update

President wa Dziko la Burkina Faso Ibrahim Traole mamawawu  wapulumuka kuchiwembu chimene  Paul-Henri Sandaogo Damiba an...
07/01/2026

President wa Dziko la Burkina Faso Ibrahim Traole mamawawu wapulumuka kuchiwembu chimene Paul-Henri Sandaogo Damiba anakonza kufuna kumuzimitsa Lero.

Paul Henri Damibiba ndi President wakale wa Burkina Faso ndipo zimamunyasa kwambiri akamaona Ibrahim chifukwa anamlanda mpando.

Lero biggy Paul anabwera okonzeka koma mission yakanika boys yao aigwila Iwo athawira Ku Ivory coast kumene amakhala

Uyu avutana naye

Ansate

A legal battle is set to ensue between coach Peter Mponda and his former bosses at FCB Nyasa Big Bullets after engaged a...
07/01/2026

A legal battle is set to ensue between coach Peter Mponda and his former bosses at FCB Nyasa Big Bullets after engaged a law firm to represent him for compensation after being fired.

The development comes just two weeks after Bullets terminated Mponda's contract after he failed to meet some of the set targets.

Mponda has engaged private practice lawyer David Kanyenda through Kanyenda, Makiyi and Associates to initiate legal proceedings.

Wayamba mavuvu sopano kufuna zake zomuchosera pantchito

Satilani Ansate kuti kuve momwe zithele

If you know you know 😅Lawyer David Kanyenda meets Peter Mponda. Ngozi! Kumati akukambilana zichani kapena yake ijaAnsant...
06/01/2026

If you know you know 😅
Lawyer David Kanyenda meets Peter Mponda. Ngozi!

Kumati akukambilana zichani kapena yake ija

Ansante

29/12/2025

📌Wanderers Youth Vs Bullets Youth
FT! Eish wafatso
Mighty Wanderers Youth 3-2 FCB Nyasa Big Bullets Youth



Address

@ Communication
Lilongwe

Telephone

+265995334650

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ansate Communication posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share