19/01/2019
Tiyambe motere pano #
Pa MBIRI YA MALAWI
Moni nonse okonda page lino.
Tingoti zonse za bwino
Mu 2019 muno.
NKHAWA
Zintha bwanji apa?
Mfumu chidzowe kuyankhula mozwanyika mtima.
Pakati pa nkhalango ya zizila mudziko la Zambia
Yomwe inali kufupi ndi tsinje wawukulu dzina lake muzizila river.
Ndikuda nkhawa kwambiri mfumu powona kuti tasala wochepa chonchi.
Zowonadi Mr mndowe'
Mfumu chidzowe nayo kusindika pangodya ya Mr mndowe.
DOKO LA SISELI
Poul kanne kulowa mu ofesi ya Mr Gibson luffer.
Zonse zantheka bwana,
Good' Mr kanne
Komano chinthu chimodzi, usayiwale pomwe ukukasinthana ndi Mr Rowland.
Akatenge 250 sojazi, malingana ndi anthu(mamonke) ambiri omwe anthawira ku nkhalango ya zizila sitingakwanitse kuwagwira, chifukwa cha masojazi tili nawo pano Mr kanne.
Chabwino bwana ndava.
ZIZILA FOREST
Mwina tiwoloke tsinjewu kupita tsidya linalo mwina nkhondoyi intha kutipezaso pano ndikutimaliza tonse mfumu chidzowe kuyankhulapo ganizo lake. Chabwino mfumu, nanga poti tsinje uja ndiwawukulu oti ambiri sangakwanise kuwagwira komaso ana Mr mndowe kutsiliramo mfundo yawo.
Eeee!! Mfundo ya bwino Mr mndowe, basi kucha kwa mawa mbandakucha aliyese aziwisidwe kuti tinkhale ndi zokambirana......
Hahaha
MBIRI YA MALAWI
Kubwera ndi m'bebe
Anthu okwana 50 perekani ndemanga zanu kuti MBIRI YA MALAWI ipitirire kapena iyime pazifukwa izi
ZIKOMO nonse.