ALL the Travellers

ALL the Travellers we travel with our hearts to heaven

when we stay in this world we must know that the world we stay is over for us to stay, we left with a short period of time so we must remind our everyday work is that belongs to God or not if not what do we think about the nearly endtime of world.

14/06/2019

Pomwe tili paulendo wopita kumwamba kodi tikudziwa kuti nthawi yatha owerenga khala maso tisangoyenda monga otsalawo koma kuchita chifuniro cha ambuye ndiko.

26/07/2017

good evening brethren do you ever think for good things that were done to you and you think did it come from

KAIN AND ABEL kain ndi abel anali ana a adam, koma anawa anali osiyana machitidwe awo, abel anali okhulupilira mulungu m...
06/04/2017

KAIN AND ABEL

kain ndi abel anali ana a adam, koma anawa anali osiyana machitidwe awo, abel anali okhulupilira mulungu muntchito zake ndipo amapereka ulemu kuchilengedwe monga mwa chilinganizo cha ambuye.

koma kain anali odzikuza ndi okonda kufunsa mafunso osonyeza kuukira nthawi zOnse pamaso pamulungu, izi zidali chonchi chifukwa cha kuchimwa kwa adam ndipo upangiri wa satana unali mwa iye.

monga mwa chikonzero cha mulungu adalora iwo kupereka nsembe yanyama kuti akhululukidwe machimo awo.

tsono inafika nthawi yoti anawa ayesedwe ndipo yeso lawo lidali lopereka nsembe pamaso pamulungu.

MUNthawi imeneyo ankayeneranso kubweretsa zoyambirila kucha za mmunda monga chopereka pamaso pamulungu.

ndipo amadziwa za ichi onse, kenako idafikanthawi yakuereka nsembe zawo ndipo abel anadza ndi nsembe yanyama paguwa lache napemphera kwamulungu ndipo anamvera iye utsika moto nunyeketsa nsembe yache .

koma kain anadza ndi zopereka zakumunda paguwa kuti zikhale nsembe yopsereza ndipo mulungu sanalandila nsembe yache nakwiira mphwache namupha.

nachoka iye ndipo mulungu anadza namfunsa kain alikuti abel mphwako? nati munandika ndikhale mlonda oyang'anira mphwanga?

ndikunva kuula kwa mphwako kuchokera kunthaka wachitiranji ichi kodi ukachita chabwino sudzalandilidwa kodi?

apa mulungu anamutemberela kain nati amene adzakhudza iwe nadzakupha adzakhala otembereredwa.

pomwepo kain anakhala mmoyo othawa thawa ndipo anadzitengera mlongo wache namka dera kummaawa kunodi. ndipo kumeneko anaberekerana ana nakhala mtundu waukulu komwe kunatuluka munthu dzina lache lameck amenenso anakwatira akwatila akazi awiri ndi wakupha uyu ndiye munthu oyamba kukwatira mitala. ndipo kunabadwa anthu ochuka ndi amphamvu potero uwu unatchedwa mtundu wa ana anthu.

03/04/2017

inali nthawi yanowa kalekalelo yomwe anauza anthu onse kuti tiseme chombo, kuti mmene mvula ikudza tipulumukiremo. koma anthu amangoseka ena kumanyoza pomwe ena amkangodutsa,

mwadzidzi kamtambo kadaoneka mlengalenga chimvula chidagwa anthu onse adafa ndipo madzi anakwera.

mtakufunsani, kodi mukadakhala mmasiku anowa kodi mukadamvera nowa, kodi simukanati bambo nowa wapenga ndindinso kuti wakalamba, mlekeni nowa poti wachita misala aseme yekha chombo ife tidzilima tigulitse timange nyumba.

ndimati mtere kuti nayonso nthawi yathu yomwe tikhalayi anthu tatanganidwa dziko lakoma, kudya kumwa makhalidwe ndizo zachuluka tiganiza kuti dziko silikutha tiganiza kuti dziko silidzatha. koma tidzadzidzimuka wakudzayo podzadza.

tiyeni tikonzeretu myoyo yathu nthawi isanathe choopsa nchakuti sitikudziwa kuti tidzafa liti?
mindful need to be on you.

God bless you all.

AMEN

26/03/2017

how are you brothers and sisters, I want to say that good news for you now is that, in travelling piriod we will meet with more difficutties that can hinder our speed, but let not our hearts be troubled as this must be done in every person`s life. good news is that soon we will see the king who was born in bethlehem, and the jews under herod they try to make him dead but the Lord`s hand was with him to protect all the way. he grew up and teach what the love is, he healed so many deases, he risen lazerous from the death, he fill the multitudes with plenty of foods, he turns water into wine, he loved the deseased people, he healed the reprosy people, he did so many things.

but all thise things that he does, the jews are not satisfyied but very angry to hime and they try to put him false words unto his mouth, until the time of betreyed by zacheous one of his decsipose, he open this way to betrayed because he new that they can fail to put him to be offender to the rules for the public.

after this they get a chance for tomenting him, he smashed, they wheeped him they talk more things to him, and theytake him to pilatto until he crucified in the cross at cavery,
in this case they look that to him its finished, but they wonder more and more to heard that he risen up from the death, they dont believe but its true that he was risen indeed.

he mat with his descsipose to the gethseman where he left to the heaven as of now he is in the right hand of the lord in heaven,

soon he will comm to take us to heaven, so as you walk with him he promise to takecare of you.

as you traval be not be dismayed whatever be tide because he will take care of you, beneeth his wings of love abide, he will take care of you through every day o`r all the night whether you want or not he still with you.

the man which I am talking about his name is Jesus christ, and he will come back as our saviour.

come now and travel together with all our hearts he will not let us fall down.

may the almighty hands of God be upon you.

all the traveller have u already bought your ticket?
24/03/2017

all the traveller have u already bought your ticket?

21/07/2016

Chatsalanso ndi chiyani choposa kuphedwa kwa oyera mtima?

Njala zivomezi ndi nkhondo zonse zakwanitsidwa tsopano.

Olalika walalika onenera wanenera okwanilitsa maulosi akwanilitsa
Maudani kaduka mkhwidzi ndi njiru zonse zachitika.

Kodi chatsala ndi chani mukamaona okondedwa?

Talimbana nako kulimbana kwabwino kwatsa mkulandira mphotho ya ntchito zathu.

Chibvumbulutso 3:15

Ndidziwa tchito zako pakuti suli otentha kapena ozizira koma uli ofunda kunalibwino ukadakhala otentha kapena ozizira.

Pamene zonse zikuchitika ife tikusankha mwadaladala kukhala ofunda.

Koma funso mkumati kodi kufunda mkutani?

Okondedwa kufunda ndiko kuti chinthucho sichozizira kapena chotentha koma chilipakatikati.

Tichulukirenji lero amkristu omwe timadzitcha kuti ndife ankhristu koma tchito zathu mzosakaniza.

Tikuchita zachikunja komaso zamapemphero nde vesilo akupitiliza kuti ndipo ine ndidzakulavula mkamwa mwanga.

Abale ndi alongo takomedwa ndi zadziko kusiya chipulumutso.

Ambuye atithandize kuti ikufza nthawi yowawitsa imene sitidzamvanso mau amulungu.
Koma mfuuuu ya oyera mtima kamba ka imfa zawo.

Pano tikumva mfuu wa azilaliki koma osawamvera idzafika nthawi tidzasakasaka mawu ake koma osawapeza.

Ndikuitanireni kukulapa okondedwa ngati mwakhala nthawi mukusowa chiyembekezo chamoyo wanu.

Idzani kwa yesu lero.

Yesu akuti

Idzani kwa ine inu nonse akulema ndi akuthodwa ndipo ine ndidzakupumulitsani.

Dziwani ichi kuti ndi nthawi yotsiliza iyi kwangotsala kanthawi pang'ono wakudzayo afika.

Waoneka kale mneneri onyenga yemwe akuchita zizindikiro ndi zozizwa zonama.

Anasintha malamulo mbuku lopatulika anasintha nyengo zoikika za yesu ngakhale mfundo zomangirira za yesu.

Tsono inu poona izi zindikirani kuti yesu alipafupi sikuti zikungochitika.

Potero lolani mitima yanu itseguke ndikuti yesu alowe mwa inu ndi inu mwa iye.

2 timoteo 4:1

Ndikuchitirani umboni pamaso pa mkristu yesu amene adzaweruza amoyo ndi akufa ndi pamaonekedwa ake ndi ufumu wake.

will u be served from this seven plagues? if u know and trust that no one can serve, there is an opened way in Jesus chr...
12/01/2016

will u be served from this seven plagues? if u know and trust that no one can serve, there is an opened way in Jesus christ just called in.his name and u shall answered. He is there because of you and me.

04/01/2016

THE FINAL WARNING
"I saw another angel come down from heaven. Having great power; and the earth was lightened with his glory. And he cried mightly with astrong voice saying, Babylon the great is fallen, is fallen, and is became the habitation of devils and the hold of every four sprit and a cage of every unclean and hatefull bird." "And I heard another voice from hevean saying, come out of her my people that ye be not partakers of her sins and that ye recieve not of her plagues." (revelation 18:1,2,4.)

This scriptures point foward to a time when the anouncements of the falling of babylon as made by the second angel of revelation 14:8
Is to be repeated with the additional mentioned of the corruption which have been entering the various organizations that consititute babylon.

Since that massage was given first in the summer of 1844.

A terrible conditions of religious world is here described.
With every rejection of truith the mind of people will come darker. There hearts are sturborn. Until they are entrenched in an infidel hardhood. In defiance of the warning which God has given, they will continue to trample upon one of the precepts of the decalogue, until they are ready to persecute thase who hold it sacred.
Christ is set at nought in the contempt placed upon his words and his people. As the teachings of spritualism are accepted by the churches. The restraint imposed upon the carnal heart is removed and the professional of religious will became a cloak to conceal the besest iniquity. A beleive in spiritual manifestations opens the door to seducing spirits and doctrins of devils and thus the influence of the evil angels will be felt in the churches.

we are now gong foward and soon we rich at the end of the time.so if we walk like people of s***m and gomora we felt to ...
29/11/2015

we are now gong foward and soon we rich at the end of the time.

so if we walk like people of s***m and gomora we felt to see the brightest morning.

those time people were drunk and drunkerdness. they make averything for they life to be well but they all fogoten that there is Lord in heaven who see them for each and every second, minute, hour, day, week , month. year and he naver sleep his eyes are on upon men's work.

Look He creared them all because of selfishness are doing like them are we fall in the drinking like them or in eating difference foods?

mmm!!!

My Lord God Almighty will he leave us doing such thing like s***m and gomora?

never done we must be carefull with our works if not mmmm

GOD WILL JUDGE.

27/11/2015

In a church queire there is agirl who always like to pass short way to home from church.

she always pass that way to and fro and that way was in the middle of the jungle.

A certain day after the practice she decided to go to home through the same way.

so she start her journey after some distance she saw a guy who stop along side of the way that she pass through.

And the girl sayed in his heart
"oh! lord help me and cover me with ur sprit of protection."

And she pass through where the guy was stoped when he reach at home she turn on the tv screen to watch after some seconds he heard that on a short way some guy was r**e ayoung girl and he was cort by the police and they showed a picture of a criminal then the girl realise that the man was the one who stoped on the way which she passed by.

Then the police men ask the qeustion to guy, and he said,

"first i saw a girl who was passed but i did nothing to her

the police men ask why?

he said that,"that girl had someone elder who walk together with her then i turn i side for them to pass.

Brethren in our travelling do we ask God to escorrt us?

look to this young girl if she wan't ask God what would happen to her.

Lets always give our hearts to God when we start our journey for him to protect us.

23/11/2015

ALL THE TRAVELLERS.

Have you all ready bought your ticket?

If that you know when you wanna have one!

us for us we have already bought jesus who is the Lord our savoiur.

I know have
my ticket
for the heaven
you need to
have tou ticket
write now.

I will move
to the
foward
in heaven never turn
backwards in heaven,
If the language of heaven will be chichewa!
I will speack chichewa in heaven,
mulibwanji mai in heaven
muli bwanji bambo in heaven.

if will chiyawo
Am gonna speak chiyawo in heaven
ajimwiche dyomba in heaven ajimwiche kusyiyeto in heaven.

if it will chilomwe mmmmm
Am gonna speak chilomwe in heaven moseliwa mapwiya in heaven moseliwa moweni in heaven.

if it will be chisena
I will speak chisena
mwaechera pai in heaven mwaecherwa nana in heaven.

if it will tumbuka
i will speak tumbuka
muli makura wadada in heaven mulimakora wankhaze in heaven.

And my driver is Jesus and my engenear is the Lord.

oh! my Lord let us prepare well to the becoming kingdom.

Address

Magalasi Road
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ALL the Travellers posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category