Dema Immigrant

Dema Immigrant Self reliant

10/03/2026

Koma ndale ndi business yotentha kuMalawi kuno

10/03/2026

The truth about the bible

Zoona zake za baibilo

1. Mulungu alipodi

2. Anthu azikhala mwa Bata ndi mtendere padziko lapansi
3. Tizipanga chilungamo nthawi zonse
4. Tiziweruzana moyenera
5. Tidzilanga wolakwa moyenera mulanduwo

18/12/2025

Technology is just a matter of kusaiwala zinsinsi za computer bas

Shupiti zako

11/12/2024

Ngat Yesu analira pa Yohane 11:35

Ine ndindan abale

05/11/2024

Danger zone
Danger environment
Danger area
Danger range
Danger surrounding
Danger campus
Danger compound
Danger outlook

Zoopsa Masiku otsiriza

09/10/2024

Nyengo ya Chaka chino ikudabwitsa ngat:

June wa 2024

June wa 2022

June wa 2019

Tapangan recall k*t kunali zotani nanunso mudabwa sure

13/08/2024

Ndale

Sizifunika phuma ngat sukuidziwa
Sizifunika chidodo ngat sukuzidziwa
Sizifunika kupusa ngat sukuzidziwa
Sizifunika kudekha kwambiri ngat sukuzidziwa
Sizifunika kupemphera
Sizifunika usatana kwambiri
Sizifunika chikondi
Sizifunika kuzitengera
Sizifunika kuzidalira
Sizifunika kuzikhulupilira

Mwachidule, ndale ndi nkhondo ngat simumadziwa

25/06/2024
01/05/2024

Amuna

06/04/2024

What if the year 2009 comes back again?
In politics
In yo family
Yo marital status
Financial stability
Education
Spiritual life
Farm yield

Mulungu atithandize

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dema Immigrant posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share