Gift Stope

Gift Stope Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Gift Stope, Shopping & retail, Klopperpark.

Tsiku lina ndinawona bambo anga akupatsa ndalama aneba 😁, nditawafusa kuti bwanji akuwapatsa ndalamayo anandiyakha kuti,...
16/07/2026

Tsiku lina ndinawona bambo anga akupatsa ndalama aneba 😁, nditawafusa kuti bwanji akuwapatsa ndalamayo anandiyakha kuti, ndalama ndizawo ndiye atha kupanganazo zomwe angafune🙆. Ine ndinangovemeleza sinapitilize kuwafusasoyi 😁🙆.

Tsiku lotsatila tinanyamuka waku Tchalitchi anandipatsa 50mt, kuti ndikapeleke 😁. Itakwana thawi yopeleka, nyimbo zinayambika😁.

Anabwela wa mbale yoyamba, bambo anga avekele.

Bambo anga: Iwe Mindo 😡, bwanji siukukapeleka??

Ine: Ndalama ndiyanga nde nditha kupanga nayo zomwe ndingafune 😁.

Madala sanapitilize kulankhula koma kukhala Duuu😁.

Kunadzabwela wa mbale yachiwili, inesso sinanyamuke kupita kukapeleka ndinangoti duuu ngati wowona za economy 😁, Bambo anga anandiyang'ana mokwiya 😡, akuti adziyakhula, ine motsitsa mau ndidangoti.

Ine: Mmmmmm madala ndati ndalama ndiyanga.

Kunabwela wa mbale yachitatu
Wa mbale yachinayi,
Wa mbale yachisanu,

Mwina wena mukudabwa kuti ndimpingo wanji umapeleka mpaka mbale zossezo 😁🤔,

Dziwani kuti iyiyi ndi History yanga nde ndikhoza kunena m'mene ndinganenele😁.

Mukakwiyasso kuti mwawelenga zopanda pake, nkwiyo ndi wanu nde kwiyani m'mene mungakwiyile😁.

Wena mwayamba kumwetulila 😁, nayo khaniyi ayi ndithu mwetulilani m'mene mungafunile pakamwa mpanu 😁.

Kaya simucomenta kapena kupanga like or kupanga follow, ndilibe nazo tchito, chifukwa foni ndiyanu nde m***a kupanga zomwe mungafune😁🤣.

21/06/2026
20/06/2026
Nenani chilungamo apa🙏🙏??Osaiwala kupanga follow Gift Stope
20/06/2026

Nenani chilungamo apa🙏🙏??

Osaiwala kupanga follow Gift Stope

Address

Klopperpark

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gift Stope posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share