20/04/2023
Okhawo amene ali oyera mtima ndiwo ana a Mulungu , kuchitila Ena zabwino kuposa kuchitiridwa.
Pitilizani kuchitila Ena zabwino . Ngati simudzatopa , mpoto mudzalandira kwa Yehovah 🙏.
# ngakhale Yesu Kristo anakanidwa ndi anthu ake pa dziko la pansi pano , nde anthu obwera kukanidwa kapena kunyozedwa sizachilendo . Chinthu chimodzi. Yesu anati mtendere ukhale kwa inu not worthy or anything of the earth. Kondan anthu obwera ndipo adzakubwezerani chikondi chomwecho . Amen 🙏